Joshua 10:3 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Motero Adonizedeki adatuma mithenga kwa Hohamu mfumu ya ku Hebroni, kwa Piramu mfumu ya ku Yaramuti, kwa Yafiya mfumu ya ku Lakisi ndi kwa Debiri mfumu ya ku Egiloni. Adatuma mau akuti,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chifukwa chake Adoni-Zedeki mfumu ya Yerusalemu anatuma kwa Hohamu, mfumu ya Hebroni, ndi kwa Piramu mfumu ya Yaramuti, ndi kwa Yafiya mfumu ya Lakisi, ndi kwa Debiri mfumu ya Egiloni, ndi kuti,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Chotsatira chake Adoni-Zedeki mfumu ya Yerusalemu inatuma uthenga kwa Hohamu mfumu ya Hebroni, Piramu mfumu ya Yarimuti, Yafiya mfumu ya Lakisi ndi Debri mfumu ya Egiloni.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cifukwa cace Adoni-Zedeki anatuma kwa Hohamu, mfumu ya Hebroni, ndi kwa Piraniu mfumu ya Yarimutu, ndi kwa Yafiya mfumu ya Lakisi, ndi kwa Dibri mfumu va Egiloni, ndi kuti,