Joshua 10:31 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Zitatha zimenezi, Yoswa pamodzi ndi ankhondo ake adapitirira kuchokera ku Libina mpaka ku Lakisi. Adazinga mzindawo ndi kuuthira nkhondo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Yoswa, ndi Aisraele onse naye, anapitirira kuchokera ku Libina kunka ku Lakisi; namanga misasa, nathira nkhondo pa uwo;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kenaka Yoswa ndi Aisraeli onse anapitirira kuchokera ku Libina kupita ku Lakisi. Iye anazungulira mzindawo ndi kuwuthira nkhondo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Yoswa, ndi Aisrayeli onse naye, anapitirira kucokera ku Libina kumka ku Lakisi; namanga misasa, nathira nkhondo pa uwo;