Joshua 10:34 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pambuyo pake Yoswa pamodzi ndi ankhondo ake adapitirira ku Lakisi mpaka ku Egiloni. Adazinga mzinda wa Egiloniwo ndi kuuthira nkhondo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Yoswa, ndi Aisraele onse naye, anapitirira kuchokera ku Lakisi mpaka ku Egiloni; namanga misasa, nathira nkhondo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kenaka Yoswa ndi Aisraeli onse anapitirira kuchokera ku Lakisi nakafika ku Egiloni. Iwo anazungulira mzindawo ndi kuwuthira nkhondo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Yoswa, ndi Aisrayeli onse naye, anapitirira kucokera ku Lakisi mpaka ku Egiloni; namanga nrisasa, nathira nkhondo.