Joshua 10:36 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono Yoswa ndi ankhondo ake adapitirira ku Egiloni mpaka kubzola mapiri, ndi kukafika ku mzinda wa Hebroni. Adauthira nkhondo,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Yoswa ndi Aisraele onse naye anakwera kuchokera ku Egiloni mpaka ku Hebroni, nauthira nkhondo;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kenaka Yoswa ndi Aisraeli onse anachoka ku Egiloni nakafika ku Hebroni ndi kukawuthira nkhondo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Yoswa ndi Aisrayeli onse naye anakwera kucokera ku Egiloni mpaka ku Hebroni, nauthira nkhondo;