Joshua 10:4 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Bwerani mudzandithandize kumenyana ndi Gibiyoni, chifukwa anthu ake apangana za mtendere ndi Yoswa ndiponso ndi Aisraele onse.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kwerani kwanga kuno, ndi kundithandiza kuti tikanthe Gibiyoni, pakuti unachitirana mtendere ndi Yoswa ndi ana a Israele.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye anatumiza mawu kuti, “Bwerani mudzandithandize kumenyana ndi Gibiyoni, chifukwa anthu ake achita pangano la mtendere ndi Yoswa ndi Aisraeli.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kwerani kwanga kuno, ndi kundithandiza kuti tikanthe Gibeoni, pakuti unacitirana mtendere ndi Yoswa ndi ana a Israyeli.