Joshua 10:42 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Yoswa adagonjetsa mafumu onseŵa pamodzi ndi dziko lao lonse kamodzinkamodzi, chifukwa choti Chauta, Mulungu wa Aisraele, ndiye amene ankaŵamenyera nkhondoyo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Yoswa anagwira mafumu awa onse ndi dziko lao nthawi yomweyi; chifukwa Yehova Mulungu wa Israele anathirira Israele nkhondo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yoswa anagonjetsa mafumu onsewa ndi kulanda dziko lawo kamodzinʼkamodzi chifukwa Yehova Mulungu wa Israeli anawamenyera nkhondo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Yoswa anagwira mafwnu awa onse ndi dziko lao nthawi yomweyi; cifukwa Yehova Mulungu wa Israyeli anathirira Israyeli nkhondo.