Joshua 10:9 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Yoswa ndi ankhondo ake adayenda usiku wonse kuchoka ku Giligala, ndipo adakathira nkhondo mwadzidzidzi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Yoswa anawadzidzimukitsa; popeza anakwera kuchokera ku Giligala usiku wonse.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Atayenda usiku wonse kuchokera ku Giligala, Yoswa anawathira nkhondo mwadzidzidzi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Yoswa anawadzidzimukitsa; popeza anakwera kucokera ku Giligala usiku wonse.