Joshua 11:1 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mbiri ya zimene zinkachitikazi idamfika Yabini, mfumu ya ku Hazori. Motero iyeyo adatumiza uthenga kwa Yobabu mfumu ya ku Madoni, ndiponso kwa mafumu a ku Simironi ndi Akisafu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo kunali, pamene Yabini mfumu ya ku Hazori anachimva, anatuma kwa Yobabu mfumu ya ku Madoni, ndi kwa mfumu ya ku Simironi, ndi kwa mfumu ya ku Akisafu,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yabini, mfumu ya Hazori, inamva zimene zinachitikazi. Tsono inatumiza uthenga kwa Yobabu mfumu ya Madoni, ndiponso kwa mafumu a ku Simironi ndi Akisafu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo kunali, pamene Yabini mfumu ya ku Hazoro anacimva, anatwna kwa Yabobu mfumu ya ku Madoni, ndi kwa mfumu ya ku Simironi, ndi kwa mfumu ya ku Akasafu,