Joshua 11:12 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Yoswa adagwira mafumu onsewo pamodzi ndi mizinda yao yomwe. Adalamula kuti aphedwe onsewo, potsata lamulo la Mose mtumiki wa Mulungu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Yoswa analanda midzi yonse ya mafumu awa, ndi mafumu ao omwe nawakantha ndi lupanga lakuthwa, nawaononga konse; monga Mose mtumiki wa Yehova adalamulira.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yoswa analanda mizinda yonse ndi mafumu ake. Anthu onse anaphedwa ndi lupanga monga momwe analamulira Mose, mtumiki wa Yehova.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Yoswa analanda midzi yonse ya mafumu awa, ndi mafumu ao omwe nawakantha ndi lupanga lakuthwa, nawaononga konse; monga Mose mtumiki wa Yehova adalamulira.