Joshua 11:18 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
atalimbana nawo nthaŵi yaitali.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Yoswa anathira nkhondo mafumu awa onse nthawi yaikulu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
atachita nawo nkhondo kwa nthawi yayitali.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Yoswa anathira nkhondo mafwnu awa onse nthawi yaikuru.