Joshua 11:2 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adatumizanso uthenga kwa mafumu a ku dziko lamapiri kumpoto kwa chigwa cha Yordani, kumwera kwa nyanja ya Galilea, m'dziko la chigwa cha Yordani ndiponso kumbali kwa nyanja, kufupi ndi Dori.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi kwa mafumu akukhala kumpoto kumapiri, ndi kuchigwa kumwera kwa Kineroti, ndi kuchidikha, ndi ku mitunda ya Dori kumadzulo;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Inatumizanso uthenga kwa mafumu a kumpoto, kumapiri, ndi mʼchigwa cha Yorodani kummwera kwa nyanja ya Kinereti, ndiponso kumadzulo mʼmbali mwa nyanja pafupi ndi Dori.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndi kwa mafwnu akukhala kumpoto kumapiri, ndi kucigwa kwumwela kwa Kineroto, ndi kucidikha, ndi ku mitunda ya Doro kwnadzulo;