Joshua 11:3 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adatumizanso uthenga kwa Akanani a pa mbali zonse ziŵiri za Yordani, kwa Aamori, Ahiti, Aperizi ndi Ayebusi a ku dziko lamapiri, mpakanso kwa Ahivi amene ankakhala patsinde pa phiri la Heremoni m'dziko la Mizipa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
kwa Akanani kum'mawa ndi kumadzulo, ndi kwa Aamori ndi Ahiti, ndi Aperizi ndi Ayebusi kumapiri, ndi kwa Ahivi kunsi kwa Heremoni, m'dziko la Mizipa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Inatumizanso uthenga kwa Akanaani amene ankakhala kummawa ndi kumadzulo kwa Yorodani. Uthenga unapitanso kwa Aamori, Ahiti, Aperezi ndi Ayebusi amene amakhala mʼdziko la ku mapiri ndiponso kwa Ahivi amene ankakhala mʼmunsi mwa phiri la Herimoni ku chigwa cha Mizipa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
kwa Akanani kwn'mawa ndi kumadzulo, ndi kwa Aamori ndi Ahiti, ndi Aperizi ndi Ayebusi kumapiri, ndi kwa Ahivi kunsi kwa Herimoni, m'dziko la Mizipa.