Joshua 12:23 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Dori (m'mbali mwa nyanja), Goimu (m'Galilea),
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
mfumu ya ku Dori, mpaka ponyamuka pa Dori, imodzi; mfumu ya ku Goimu m'Galileya, imodzi;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
mfumu ya Dori ku Nafoti Dori — imodzi mfumu ya Goyini ku Giligala — imodzi
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
mfumuya ku Doro, mpaka ponyamuka pa Doro, imodzi; mfumu ya ku Goimu m'Giligala, imodzi;