Joshua 12:3 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Dzikolo lidaphatikizaponso chigwa cha Yordani, kuyambira kumwera kwa nyanja ya Galilea, kumapita cha ku Beteyesimoti, mzinda umene uli pafupi pa Nyanja Yakufa, mpaka kumwera ndithu, patsinde pa phiri la Pisiga.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi pachidikha mpaka nyanja ya Kineroti kum'mawa, ndi mpaka nyanja ya kuchidikha, ndiyo Nyanja ya Mchere kum'mawa, njira ya Beteyesimoti; ndi kumwera pansi pa matsikiro a Pisiga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye ankalamuliranso dera la chigwa cha Yorodani kuyambira ku Nyanja ya Kinereti, kummawa ndi kumatsika mpaka ku Beti-Yesimoti, mzinda umene unali kummawa kwa Nyanja ya Mchere ndi kutsikabe kummwera mpaka pa tsinde pa phiri la Pisiga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndi pacidikha mpaka nyanja ya Kineroti kum'mawa, ndi mpaka nyanja ya kucidikha, ndiyo Nyanja ya Mcere kum'mawa, njira ya Beti-Yesimoti; ndi kumwela pansi pa matsikiro a Pisiga.