Joshua 12:4 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Aisraele adagonjetsanso Ogi, mfumu ya ku Basani, amene anali mmodzi mwa otsala a Arefaimu. Iyeyu ankakhala ku Asitaroti ndi ku Ederei.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nalandanso malire a Ogi mfumu ya Basani wotsala wa Arefaimu, wokhala ku Asitaroti ndi ku Ederei,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ogi mfumu ya mzinda wa Basani, amene anali mmodzi mwa otsala mwa Arefaimu. Iye ankakhala ku Asiteroti ndi Ederi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nalandanso malire a Ogi mfumu ya Basana wotsala wa Arefai, wokhala ku Asitarotu ndi ku Edrei,