Joshua 12:9 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mafumu amene adagonjetsedwawo ndi aŵa: mafumu a ku Yeriko, Ai pafupi ndi Betele,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
mfumu ya ku Yeriko, imodzi; mfumu ya ku Ai, ndiwo m'mbali mwa Betele, imodzi;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
mfumu ya Yeriko — imodzi mfumu ya Ai (kufupi ndi Beteli — imodzi
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
mfumu ya ku Yeriko, imodzi; mfumu ya ku Ai, ndiwo m'mbali mwa Beteli, imodzi;