Joshua 13:10 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Linkaphatikizaponso mizinda yonse yomwe inkalamulidwa ndi Sihoni mfumu ya Aamori, amene ankalamula ku Hesiboni, mpaka ku malire a Aamoni.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi midzi yonse ya Sihoni mfumu ya Aamori, wakuchita ufumu m'Hesiboni, mpaka malire a ana a Amoni;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Linkaphatikizanso mizinda yonse ya mfumu Sihoni ya Aamori, imene inkalamulira mu Hesiboni, mpaka ku malire a Aamoni.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndi midzi yonse ya Sihoni mfumu ya Aamori, wakucita ufumu m'Hesiboni, mpaka malire a ana a Amoni;