Joshua 13:11 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Lidaphatikizaponso Giliyadi ndi dziko limene Agesuri ndi Amakati ankakhalamo, kudzanso phiri lonse la Heremoni, pamodzi ndi Basani, mpaka ku Saleka.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi Giliyadi, ndi malire a Agesuri, ndi Amaakati, ndi phiri lonse la Heremoni, ndi Basani lonse mpaka ku Saleka;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Dzikoli linaphatikizanso Giliyadi, dziko la anthu a ku Gesuri ndi Maaka, phiri lonse la Herimoni ndi dziko lonse la Basani mpaka ku Saleka.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndi Gileadi, ndi malire a Agesuri, ndi Amaakati, ndi phiri lonse la Herimoni, ndi Basana ionse mpaka ku Saleka;