Joshua 13:15 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mose adapereka gawo lina la dziko kwa mabanja a fuko la Rubeni kuti likhale choloŵa chao.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Mose anapatsira fuko la ana a Rubeni monga mwa mabanja ao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mose anapereka gawo lina la dziko kwa mabanja a fuko la Rubeni.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Mose anapatsira pfuko la ana a Rubeni monga mwa mabanja ao.