Joshua 13:17 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
kuphatikizapo Hesiboni, pamodzi ndi mizinda yonse ya ku chigwa monga: Diboni, Bamoti-Baala, Bete-Baala-Meyani,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Hesiboni ndi midzi yake yonse yokhala pachidikha; Diboni, ndi Bamoti-Baala ndi Bete-Baala-Meoni;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Dzikolo linaphatikizanso Hesiboni ndi mizinda yake yonse, komanso mizinda monga Diboni, Bamoti Baala, Beti-Baala-Meoni,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Hesiboni ndi midzi yace yonse yokhala pacidikha; Diboni, ndi Bamoto-baala ndi Betibaala-Meoni;