Joshua 13:22 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pakati pa ophedwa ndi Aisraele panali Balamu, mwana wa Beori, wolosa zakutsogolo uja.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ana a Israele anaphanso ndi lupanga Balamu mwana wa Beori, mlauli uja, pamodzi ndi ena adawaphawo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kuwonjezera pa amene anaphedwa ndi nkhondo, Aisraeli anapha ndi lupanga Balaamu mwana wa Beori, amene amachita za matsenga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ana a Israyeli anaphanso ndi lupanga Balamu mwana wa Beori, mlauli uja, pamodzi ndi ena adawaphawo.