Joshua 13:24 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Gawo lina la dzikolo, Mose adalipatsa mabanja a fuko la Gadi, kuti likhale choloŵa chao.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Mose anapatsira fuko la Gadi, ana a Gadi, monga mwa mabanja ao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Dera limene Mose anapereka kwa mabanja a fuko la Gadi ndi ili:
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Mose anapatsira pfuko la Gadi, ana a Gadi, monga mwa mabanja ao.