Joshua 13:26 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Lidayambira ku Hesiboni mpaka ku Ramati-Mizipe ndi Betonimu, kuchokeranso ku Mahanaimu mpaka ku malire a Lodebara.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi kuyambira Hesiboni mpaka Ramati-Mizipe, ndi Betonimu; ndi kuyambira Mahanaimu mpaka malire a Debiri;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
ndiponso kuyambira ku Hesiboni mpaka ku Ramati-Mizipa, ndi Betonimu; ndiponso kuyambira ku Mahanaimu mpaka ku dziko la Debri.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndi kuyambira Hesiboni mpaka Ramati-Mizipe, ndi Betonimu; ndi kuyambira Mahanaimu mpaka malire a Dibiri;