Joshua 13:28 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mizinda imeneyi, pamodzi ndi midzi yake, ndiyo imene idapatsidwa kwa mabanja a fuko la Gadi, kuti ikhale choloŵa chao.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ichi ndi cholowa cha ana a Gadi, monga mwa mabanja ao, midzi yake ndi milaga yake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mizinda ndi midzi imeneyi inali cholowa cha mabanja a fuko la Gadi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ici ndi colowa ca ana a Gadi, monga mwa mabanja ao, midzi yace ndi miraga yace.