Joshua 13:30 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Dzikolo lidayambira ku Mahanaimu kuphatikizapo dziko lonse la mfumu Ogi, mfumu ya ku Basani, pamodzi ndi midzi 60 ya ku Yairo, ku Basaniko.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo malire ao anayambira ku Mahanaimu, Basani lonse, ufumu wonse wa Ogi mfumu ya ku Basani, ndi midzi yonse ya Yairi, yokhala m'Basani, midzi makumi asanu ndi limodzi;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Derali linayambira ku Mahanaimu kuphatikizapo dziko lonse la mfumu Ogi, Mfumu ya ku Basani, pamodzi ndi mizinda 60 ya ku Yairi, ku Basaniko.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo malire ao anayambira ku Mahanaimu, Basana lonse, ufumu wonse wa Ogi mfumu ya ku Basana, ndi midzi yonse ya Yairi, yokhala m'Basana, midzi makumi asanu ndi limodzi;