Joshua 13:4 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Palinso dziko la Akanani ndi la Meala, lomwe lili m'manja mwa Asidoni mpaka ku Afeki, malo amene ali pafupi ndi malire a Aamori.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
kumwera dziko lonse la Akanani, ndi Meara ndiwo wa Asidoni, mpaka ku Afeki, mpaka ku malire a Aamori;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Dziko lina la Akanaani ndi Ameara limene lili mʼmanja mwa Asidoni mpaka ku Afeki, dziko limene linachitana malire ndi dziko la Aamori.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
kumwela dziko lonse la Akanani, ndi Meara ndiwo wa Asidoni, mpaka ku Afeka, mpaka ku malire a Aaroori;