Joshua 13:5 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Palinso dziko lonse la Gebala ndi la Lebanoni chakuvuma, kuchokera ku Balagadi patsinde pa phiri la Heremoni mpaka ku Hamatipasi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi dziko la Agebala, ndi Lebanoni, lonse kum'mawa, kuyambira Baala-Gadi pa tsinde la phiri la Heremoni, mpaka polowera pake pa Hamati;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Palinso dziko lonse la Gebala ndi Lebanoni cha kummawa kuyambira ku Baala-Gadi pa tsinde pa phiri la Herimoni mpaka ku Lebo Hamati.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndi dziko la Agebili, ndi Lebano lonse kum'mawa, kuyambira Baala-gadi pa tsinde la phiri la Herimoni, mpaka polowera pace pa Hamati;