Joshua 13:7 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono ugaŵe maiko ameneŵa pakati pa mafuko asanu ndi anai ndi theka lina lija la fuko la Manase, kuti akhale choloŵa chao.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo tsopano uwagawire mafuko asanu ndi anai, ndi fuko la Manase logawika pakati, dziko ili likhale cholowa chao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsopano ugawire dziko limeneli mafuko asanu ndi anayi ndiponso theka la fuko la Manase, kuti likhale cholowa chawo.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo tsopano uwagawire mapfuko asanu ndi anai, ndi pfuko la Manase logawika pakati, dziko ili likhale colowa cao.