Joshua 14:13 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamenepo Yoswa adadalitsa Kalebe, mwana wa Yefune, nampatsa Hebroni kuti likhale dziko lake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamenepo Yoswa anamdalitsa, napatsa Kalebe mwana wa Yefune Hebroni likhale cholowa chake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo Yoswa anadalitsa Kalebe mwana wa Yefune ndi kumupatsa Hebroni kukhala dziko lake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamenepo Yoswa anamdalitsa, napatsa Kalebe mwana wa Yefune Hebroni likhale colowa cace.