Joshua 14:3 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mose adagaŵira mafuko aŵiri ndi theka aja magawo ao a dziko kuvuma kwa Yordani, koma Alevi okha sadaŵagaŵire.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti Mose adapatsa mafuko awiri, ndi fuko logawika pakati, cholowa tsidya ilo la Yordani; koma sanapatse Alevi cholowa pakati pao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mose anapereka kwa mafuko awiri ndi theka dziko la kummawa kwa Yorodani, koma fuko la Levi lokha silinagawiridwe malo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti Mose adapatsa mapfuko awiri, ndi pfuko logawika pakati, colowa tsidya ito la Yordano; koma sanapatsa Alevi colowa pakati pao,