Joshua 14:9 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamenepo Mose adandilonjeza kuti, ‘Chifukwa choti wamvera mokhulupirika Chauta, Mulungu wanga, iweyo pamodzi ndi ana ako, udzalandiradi dziko limene walipondalo, kuti likhale choloŵa chako.’ ”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Mose analumbira tsiku lomwelo ndi kuti, Zedi, dzikoli phazi lako lapondapo lidzakhala cholowa chako, ndi cha ana ako kosalekeza, chifukwa unatsata Yehova Mulungu wanga ndi mtima wonse.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kotero tsiku limenelo Mose anandilonjeza kuti, ‘Dziko limene unayendamo lidzakhala lako ndiponso la ana ako kwamuyaya chifukwa unamvera Yehova Mulungu wanga ndi mtima wako wonse.’
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Mose analumbira tsiku lomwelo ndi kuti, Zedi, dzikoli phazi lako lapondapo lidzakhala colowa cako, ndi ca ana ako kosalekeza, cifukwa unatsata Yehova Mulungu wanga ndi mtima wonse.