Joshua 16:5 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Dziko la mabanja a Efuremu ndi ili: malire ake akuvuma anali Ataroti-Adara mpaka kukafika kumtunda kwake kwa Betehoroni.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo malire a ana a Efuremu, monga mwa mabanja ao, ndiwo: malire a cholowa chao kum'mawa ndiwo Ataroti-Adara, mpaka Betehoroni wa kumtunda;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Dziko la mabanja a fuko la Efereimu ndi ili: Malire a dzikolo anachokera kummawa kwa Ataroti Adari mpaka ku mtunda kwa Beti-Horoni.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo malire a ana a Efraimu, monga mwa mabanja ao, ndiwo: malire a colowa cao kum'mawa ndiwo Atarotu-Adara, mpaka Betihoroni wa kumtunda;