Joshua 16:7 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono kuchokera ku Yanowa, adatsikira ku Ataroti ndi ku Naara. Adakafika ku Yeriko ndi kukathera m'Yordani.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
natsika kuchokera ku Yanowa, kunka ku Ataroti, ndi ku Naara, nafika ku Yeriko, natuluka ku Yordani.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo kuchokera ku Yanowa anatsikira ku Ataroti ndi Naara, nakafika ku Yeriko ndi kukathera ku mtsinje wa Yorodani.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
natsika kucokera ku Yanoa, kumka ku Atarotu, ndi ku Naara, nafika ku Yeriko, naturuka ku Yordano.