Joshua 16:9 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
kuphatikizapo mizinda ndi midzi yopatsidwa kwa Aefuremu, koma yokhala m'kati mwa dziko la anthu a fuko la Manase.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
pamodzi ndi midzi adaipatulira ana a Efuremu pakati pa cholowa cha ana a Manase, midzi yonse pamodzi ndi milaga yao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
kuphatikizapo mizinda yonse ndi midzi yake yopatsidwa kwa Efereimu, koma yokhala mʼkati mwa dziko la Manase.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
pamodzi ndi midzi adaipatulira ana a Efraimu pakati pa colowa ca ana a Manase, midzi yonse pamodzi ndi miraga yao.