Joshua 17:13 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ngakhale pamene Aisraele anali amphamvu m'dzikomo, sadapirikitse Akanani onse, koma adangoŵasandutsa anthu ogwira ntchito yathangata.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo kunali pamene ana a Israele atakula mphamvu anasonkhetsa Akanani osawaingitsa onse.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ngakhale Aisraeli anali a mphamvu mʼdzikomo, sanapirikitse Akanaani onse koma anangowasandutsa kukhala akapolo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo kunali pamene ana a lsrayeli atakula mphamvu anasonkhetsa Akanani osawaingitsa onse.