Joshua 17:5 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Choncho kuwonjeza pa maiko a Giliyadi ndi Basani a kuvuma kwa Yordani, a fuko la Manase adalandiranso magawo khumi,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anamgwera Manase magawo khumi, osawerenga dziko la Giliyadi ndi Basani lokhala tsidya lija la Yordani:
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Choncho kuwonjezera pa mayiko a Giliyadi ndi Basani kummawa kwa Yorodani, anthu a fuko la Manase analandiranso magawo khumi
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anamgwera Manase magawo khumi, osawerenga dziko la Gileadi ndi Basana lokhala tsidya lija la Yordano: