Joshua 17:8 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Dzikolo linali la Manase, koma mzinda wa Tapuwa wapamalire unali wa fuko la Efuremu, ngakhale kuti m'pakati penipeni pa mizinda ya Manase.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Dziko la Tapuwa linali la Manase; koma Tapuwa mpaka malire a Manase linakhala la ana a Efuremu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
(Manase anatenga dziko la Tapuwa, koma mzinda wa Tapuwawo, umene unali mʼmalire mwa Manase unali wa fuko la Efereimu).
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Dziko la Tapua linali la Manase; koma Tapua mpaka malire a Manase linakhala la ana a Efraimu.