Joshua 18:11 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mabanja a fuko la Benjamini adalandira dziko la pakati pa Yuda ndi Yosefe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo maere a fuko la ana a Benjamini anakwera monga mwa mabanja ao; ndi malire a gawo lao anatuluka pakati pa ana a Yuda ndi ana a Yosefe.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Maere anagwera mabanja a fuko la Benjamini. Dziko limene anapatsidwa linali pakati pa fuko la Yuda ndi fuko la Yosefe:
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo maere a ana a Benjamini anakwera monga mwa mabanja ao; ndi malire a gawo lao anaturuka pakati pa ana a Yuda ndi ana a Yosefe.