Joshua 18:21 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mizinda ya mabanja a Benjamini inali Yeriko, Betehogila, Emekezizi,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma midzi ya fuko la ana a Benjamini monga mwa mabanja ao ndiyo Yeriko, ndi Betehogila, ndi Emekezizi;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mabanja a fuko la Benjamini anali ndi mizinda iyi; Yeriko, Beti-Hogila, Emeki Kezizi,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma midzi ya pfuko la ana a Benjamini monga mwa mabanja ao ndiyo Yeriko, ndi Beti-hogila, ndi Emekikozizi;