Joshua 19:11 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono malirewo adakwera naloŵa kuzambwe ku Mareyala, nakafika ku Debeseti ndi ku mtsinje wa kuvuma kwa Yokoneamu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
nakwera malire ao kunka kumadzulo ndi ku Mareyala nafikira ku Dabeseti, nafikira ku mtsinje wa patsogolo pa Yokoneamu;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Malirewo anakwera kupita cha kumadzulo ku Marala nakafika ku Dabeseti ndi ku mtsinje wa kummawa kwa Yokineamu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
nakwera malire ao kumka kumadzulo ndi ku Marala nafikira ku Dabeseti, nafikira ku mtsinje wa patsogolo pa Yokineamu;