Joshua 19:12 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pa mbali ina ya Saridi adapita chakuvuma ku malire a Kisiloti-Tabori, mpaka ku Debarati, nakafika ku Yafiya.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi kuchokera ku Saridi anazungulira kunka kum'mawa kumatulukira dzuwa, mpaka malire a Kisiloti-Tabori; natuluka kunka ku Daberati, nakwera ku Yafiya;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kuchokera ku mbali ina ya Saridi malire anakhota kupita kummawa ku malire a Kisiloti-Tabori mpaka ku Daberati nakwera mpaka ku Yafiya.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndi kucokera ku Saridi anazungulira kumka kum'mawa kumaturukira dzuwa, mpaka malire a Kisilotu-tabori; naturuka kumka ku Daberati, nakwera ku Yafia;