Joshua 19:13 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kuchokera kumeneko, adabzola naloŵa chakuvuma kumapita ku Gatihefere ndi ku Etikazini, kuloŵa ku Neya njira yaku Rimoni.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi pochoka pamenepo anapitirira kunka kum'mawa ku Gatihefere, ku Etikazini; natuluka ku Rimoni umene ulembedwa mpaka ku Neya,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kuchokera kumeneko anabzola kulowa cha kummawa mpaka ku Gati-Heferi ndi ku Eti Kazini ndi kumaloza ku Neya njira ya ku Rimoni.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndi pocoka pamenepo anapitirira kumka kum'mawa ku Gati-heferi, ku Etikazini; naturuka ku Remoni umene ulembedwa mpaka ku Nea,