Joshua 19:14 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kumpoto malire amenewo adapita molunjika ku Hanatoni, nakathera ku chigwa cha Ifutahele.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
nauzungulira malire kumpoto, kunka ku Hanatoni; ndi matulukiro ake anali ku chigwa cha Ifutahele;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mbali ya kumpoto malirewo analoza ku Hanatoni ndipo anakathera ku chigwa cha Ifita Eli.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
nauzungulira malire kumpoto, kumka ku Hanatoni; ndi maturukiro ace anali ku cigwa ca Ifita-eli;