Joshua 19:16 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mizinda imeneyi pamodzi ndi midzi yake inali m'dziko limene mabanja a fuko la Zebuloni adalandira ngati choloŵa chao.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ichi ndi cholowa cha ana a Zebuloni monga mwa mabanja ao, midzi iyi ndi milaga yao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mizinda imeneyi pamodzi ndi midzi yake ndi imene mabanja a fuko la Zebuloni analandira.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ici ndi colowa ca ana a Zebuloni monga mwa mabanja ao, midzi iyi ndi miraga yao.