Joshua 19:23 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mizinda imeneyi, pamodzi ndi midzi yakeyo, inali m'dziko limene mabanja a fuko la Isakara adalandira ngati choloŵa chao.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ichi ndi cholowa cha fuko la ana a Isakara, monga mwa mabanja ao, midzi ndi milaga yao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mizinda imeneyi pamodzi ndi midzi yake ndiyo inali cholowa cha mabanja a fuko la Isakara.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ici ndi colowa ca pfuko la ana a Isakara, monga mwa mabanja ao, midzi ndi miraga yao.