Joshua 19:8 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Imeneyi idaphatikizapo midzi yozungulira mizindayo, mpaka kukafika ku Baala-Tibere, ndiye kuti Rama wakumwera. Dziko limeneli ndi limene mabanja a fuko la Simeoni adalandira kukhala choloŵa chao.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi milaga yonse yozungulira midzi iyi mpaka Baalati-Bere ndiwo Rama kumwera. Ndicho cholowa cha fuko la ana a Simeoni, monga mwa mabanja ao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Dzikolo linaphatikizanso midzi yonse yozungulira mizinda imeneyi mpaka ku Baalati-Beeri, ndiye kuti Rama wa kummwera. Ili ndi dziko limene mabanja a fuko la Simeoni analandira kukhala lawo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndi miraga yonse yozungulira midzi iyi mpaka Baalata-beeri ndiwo Rama kumwera. Ndico colowa ca pfuko la ana a Simeoni, monga mwa mabanja ao.