Joshua 2:11 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Titangomva zimenezi, tonsefe tidataya mtima, ndipo mantha adatigwira kukuwopani inu. Tikudziŵa kuti Chauta, Mulungu wanu, ndiye Mulungu wa kumwamba ndi dziko lonse lapansi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo titamva ichi mitima yathu inasungunuka; analibenso mtima ndi mmodzi yense, chifukwa cha inu; pakuti Yehova Mulungu wanu, ndiye Mulungu wa m'mwamba umo, ndi pa dziko lapansi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Titamva zimenezi, ife tinataya mtima ndipo aliyense wa ife ali ndi mantha chifukwa cha inu. Tikudziwa kuti Yehova Mulungu wanu ndi Mulungu wa kumwamba ndi dziko lapansi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo titamva ici mitima yathu inasungunuka; anahbenso mtima ndi mmodzi yense, cifukwa ca inu; pakuti Yehova Mulungu wanu, ndiye Mulungu wa m'mwamba umo, ndi pa dziko lapansi.