Joshua 2:13 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Bambo wanga, mai wanga, pamodzi ndi alongo anga, abale anga ndi mabanja ao omwe, tonsefe mudzatisungire moyo, musadzatiphe.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
kuti mudzawasunga ndi moyo atate wanga ndi mai wanga, ndi alongo anga ndi abale anga, ndi zonse ali nazo, ndi kupulumutsa miyoyo yathu kuimfa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Inu mulonjeze kuti simudzapha abambo anga ndi amayi anga, abale anga ndi alongo anga ndi mabanja awo omwe.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
kuti mudzawasunga ndi moyo atate wanga ndi mai wanga, ndi alongo anga ndi abale anga, ndi zonse ali nazo, ndi kupulumutsa miyoyo yathu kuimfa.