Joshua 2:14 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthuwo adamuyankha kuti, “Ife tili okonzeka kufa kuti tikupulumutse iwe. Ukapanda kuulula zimene tachitazi, ifenso tidzasunga lonjezo lathu ndi iwe mokhulupirika, Chauta akadzatipatsa dzikoli.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo amunawo anati kwa iye, Moyo wathu ndiwo moyo wanu, mukapanda kuwulula chodzera ife; ndipo kudzakhala kuti, pakutipatsa ife dziko ili Yehova, tidzakuchitira chifundo ndi choonadi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anthuwo anamuyankha kuti, “Ife ndife okonzeka kufa chifukwa cha inu. Ngati iwe sudzawulula zimene tachitazi, ndiye kuti ife tidzakukomera mtima ndi kusunga pangano lathu ndi iwe, Yehova akadzatipatsa dziko lino.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo amunawo anati kwa iye, Moyo wathu ndiwo moyo wanu, mukapanda kuulula codzera ife; ndipo kudzakhala kuti, pakutipatsa ife dziko ili Yehova, tidzakucitira cifundo ndi coonadi.