Joshua 2:15 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nyumba ya Rahabuyo idaali pa linga la mzindawo. Motero azondiwo atatulukira pa windo, Rahabu adaŵatsitsa pansi ndi chingwe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamenepo anawatsitsa pazenera ndi chingwe; popeza nyumba yake inali pa linga la mudzi, nakhala iye palingapo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Popeza nyumba ya Rahabe inali pa linga la mzindawo, azondi aja anatulukira pa zenera. Rahabe anawatsitsa pansi ndi chingwe.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamenepo anawatsitsa pazenera ndi cingwe; popeza nyumba yace lnali pa linga La mudzi, nakhala iye palingapo.